Mateyu 28:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Atafika pafupi, anazindikira kuti pachitika chivomezi champhamvu, pakuti mngelo wa Yehova anatsika kumwamba, ndipo anafika ndi kugubuduza chimwala chija, n’kukhala pachimwalapo.+ Yohane 1:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Anamuuzanso kuti: “Ndithudi ndikukuuzani anthu inu, mudzaona kumwamba kutatseguka, angelo+ a Mulungu akukwera ndi kutsikira kwa Mwana wa munthu.”+ Aheberi 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kodi angelo onse si mizimu+ yotumikira ena,+ yotumidwa kukatumikira amene adzalandire chipulumutso monga cholowa chawo?+
2 Atafika pafupi, anazindikira kuti pachitika chivomezi champhamvu, pakuti mngelo wa Yehova anatsika kumwamba, ndipo anafika ndi kugubuduza chimwala chija, n’kukhala pachimwalapo.+
51 Anamuuzanso kuti: “Ndithudi ndikukuuzani anthu inu, mudzaona kumwamba kutatseguka, angelo+ a Mulungu akukwera ndi kutsikira kwa Mwana wa munthu.”+
14 Kodi angelo onse si mizimu+ yotumikira ena,+ yotumidwa kukatumikira amene adzalandire chipulumutso monga cholowa chawo?+