Genesis 16:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Tsopano Sarai, mkazi wa Abulamu, sanamuberekere ana.+ Koma Saraiyo anali ndi kapolo wake Mwiguputo, dzina lake Hagara.+ Genesis 30:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Leya ataona kuti wasiya kubereka, anapereka kapolo wake Zilipa kwa Yakobo kuti akhale mkazi wake.+ Genesis 46:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Amenewa ndiwo anali ana a Zilipa,+ yemwe Labani anam’pereka kwa mwana wake wamkazi Leya. Ndiwo ana amene Zilipa anaberekera Yakobo m’kupita kwa nthawi. Onse pamodzi analipo 16.
16 Tsopano Sarai, mkazi wa Abulamu, sanamuberekere ana.+ Koma Saraiyo anali ndi kapolo wake Mwiguputo, dzina lake Hagara.+
18 Amenewa ndiwo anali ana a Zilipa,+ yemwe Labani anam’pereka kwa mwana wake wamkazi Leya. Ndiwo ana amene Zilipa anaberekera Yakobo m’kupita kwa nthawi. Onse pamodzi analipo 16.