Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 35:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Ana amene Biliha kapolo wa Rakele anaberekera Yakobo anali Dani ndi Nafitali.

  • Genesis 46:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Ana a Nafitali+ anali Yahazeeli, Guni,+ Yezera ndi Silemu.+

  • Genesis 49:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 “Nafitali+ ndi mbawala yaikazi yopepuka miyendo, ndipo amanena mawu okoma.+

  • Deuteronomo 33:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Ndipo kwa Nafitali anati:+

      “Nafitali wakhutira chifukwa chovomerezedwa ndi Yehova,

      Ndipo madalitso Ake amuchulukira.

      Tenga chigawo cha kumadzulo ndi kum’mwera.”+

  • Chivumbulutso 7:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Mu fuko la Aseri,+ 12,000.

      Mu fuko la Nafitali,+ 12,000.

      Mu fuko la Manase,+ 12,000.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena