Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 32:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Pa chifukwa chimenechi, ana a Isiraeli sadya mnyewa wa pansukunyu kufikira lero, chifukwa ndi umene munthu uja anagwira pogulula nsukunyu ya Yakobo.+

  • 2 Akorinto 12:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Chifukwa cha kuchuluka kwa mauthenga amene anaululidwa kwa ine, aliyense asandiganizire koposa mmene ayenera kundiganizira.

      Chotero, kuti ndisadzikweze mopitirira muyezo,+ ndinapatsidwa munga m’thupi,+ mngelo wa Satana woti azindimenya nthawi zonse, kuti ndisadzikweze mopitirira muyezo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena