Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Akorinto 12
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

2 Akorinto 12:1

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 2:17; 22:17

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    12/2018, tsa. 8

2 Akorinto 12:2

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Eze 8:3

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 12

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    12/2018, tsa. 8

    Nsanja ya Olonda,

    12/15/2004, tsa. 30

    10/15/2004, ptsa. 8-10

    7/15/2000, tsa. 27

2 Akorinto 12:3

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Eze 3:14

2 Akorinto 12:4

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aef 1:3

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    12/2018, tsa. 8

    Nsanja ya Olonda,

    7/15/2015, ptsa. 8-9

    7/15/2008, tsa. 28

    10/15/2004, ptsa. 8-10

    6/15/1997, tsa. 5

2 Akorinto 12:5

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +2Ak 11:30

2 Akorinto 12:6

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +2Ak 10:8; 11:16

2 Akorinto 12:7

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Miy 16:18
  • +Aga 4:13

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    11/2019, ptsa. 8-9

    Utumiki Komanso Moyo Wathu,

    5/2019, tsa. 4

    Nsanja ya Olonda,

    4/1/2014, tsa. 5

    6/15/2008, ptsa. 3-4

    12/15/2006, tsa. 24

    8/15/2006, tsa. 21

    8/1/2005, ptsa. 21-22

    2/15/2002, ptsa. 13-14

    3/1/2000, tsa. 4

    6/1/1997, tsa. 25

    9/15/1990, tsa. 27

    11/15/1987, tsa. 29

    Kingdom Ministry,

    5/1998, tsa. 1

    Galamukani!,

    6/8/1997, ptsa. 14-15

2 Akorinto 12:8

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Pe 5:7

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    11/2019, tsa. 9

    Nsanja ya Olonda,

    4/1/2014, tsa. 5

    1/1/2009, tsa. 30

    12/15/2006, tsa. 24

    11/15/1987, tsa. 29

2 Akorinto 12:9

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +De 3:26
  • +Yes 40:29; Ahe 11:34
  • +2Ak 11:30

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    7/2020, ptsa. 14-19

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    11/2019, tsa. 9

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    1/2018, tsa. 9

    Nsanja ya Olonda,

    6/15/2008, tsa. 6

    12/15/2006, tsa. 24

    8/1/2005, ptsa. 21-22

    2/15/2002, ptsa. 18-19

    3/1/2000, tsa. 4

    6/1/1997, ptsa. 25-26

    11/15/1987, tsa. 29

    6/1/1986, tsa. 12

    Galamukani!,

    6/8/1997, ptsa. 14-15

2 Akorinto 12:10

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Afi 4:13

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    7/2020, ptsa. 14-19

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    1/2018, tsa. 9

    Nsanja ya Olonda,

    3/15/2010, tsa. 18

    6/15/2008, ptsa. 3-4, 6

    9/15/2004, ptsa. 13-14

2 Akorinto 12:11

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +2Ak 12:1
  • +2Ak 11:5; Chv 2:2
  • +2Ak 11:23

2 Akorinto 12:12

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Ak 9:2
  • +2Ak 6:4
  • +Mac 14:3; 15:12; Aro 15:19

2 Akorinto 12:13

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Ak 9:12; 2Ak 11:9

2 Akorinto 12:14

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +2Ak 13:1
  • +Mac 20:33
  • +1Ak 4:14; Aga 4:19
  • +Miy 13:22; 19:14

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    8/15/1997, tsa. 20

    10/1/1996, tsa. 29

    6/15/1987, ptsa. 25, 26-27

    2/1/1987, tsa. 5

2 Akorinto 12:15

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Miy 11:30; 2Ak 1:6; Afi 2:17; Akl 1:24; 1At 2:8; Ahe 13:17

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Utumiki wa Ufumu,

    6/2007, tsa. 1

    Nsanja ya Olonda,

    11/15/2000, tsa. 21

    9/15/2000, ptsa. 22-23

2 Akorinto 12:16

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +2Ak 11:9
  • +2Ak 7:2

2 Akorinto 12:18

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +2Ak 8:6, 16
  • +Afi 1:27

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    5/1/1988, ptsa. 16-17

2 Akorinto 12:19

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Ak 10:33

2 Akorinto 12:20

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +2Ak 10:2; 13:2
  • +1Ak 3:3
  • +Afi 2:3

2 Akorinto 12:21

Mawu a M'munsi

  • *

    Onani Zakumapeto 7.

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Ak 5:1; 2Ak 2:2
  • +1Ak 6:9, 13
  • +Aro 13:13; Aga 5:19; Aef 4:19; 2Pe 2:2; Yuda 4

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    3/15/2012, tsa. 31

Mabaibulo Ena

Dinani pa nambala ya vesi kuti muone mavesi a m'Baibulo lina ofanana ndi vesilo.

Malemba Ena

2 Akor. 12:1Mac 2:17; 22:17
2 Akor. 12:2Eze 8:3
2 Akor. 12:3Eze 3:14
2 Akor. 12:4Aef 1:3
2 Akor. 12:52Ak 11:30
2 Akor. 12:62Ak 10:8; 11:16
2 Akor. 12:7Miy 16:18
2 Akor. 12:7Aga 4:13
2 Akor. 12:81Pe 5:7
2 Akor. 12:9De 3:26
2 Akor. 12:9Yes 40:29; Ahe 11:34
2 Akor. 12:92Ak 11:30
2 Akor. 12:10Afi 4:13
2 Akor. 12:112Ak 12:1
2 Akor. 12:112Ak 11:5; Chv 2:2
2 Akor. 12:112Ak 11:23
2 Akor. 12:121Ak 9:2
2 Akor. 12:122Ak 6:4
2 Akor. 12:12Mac 14:3; 15:12; Aro 15:19
2 Akor. 12:131Ak 9:12; 2Ak 11:9
2 Akor. 12:142Ak 13:1
2 Akor. 12:14Mac 20:33
2 Akor. 12:141Ak 4:14; Aga 4:19
2 Akor. 12:14Miy 13:22; 19:14
2 Akor. 12:15Miy 11:30; 2Ak 1:6; Afi 2:17; Akl 1:24; 1At 2:8; Ahe 13:17
2 Akor. 12:162Ak 11:9
2 Akor. 12:162Ak 7:2
2 Akor. 12:182Ak 8:6, 16
2 Akor. 12:18Afi 1:27
2 Akor. 12:191Ak 10:33
2 Akor. 12:202Ak 10:2; 13:2
2 Akor. 12:201Ak 3:3
2 Akor. 12:20Afi 2:3
2 Akor. 12:211Ak 5:1; 2Ak 2:2
2 Akor. 12:211Ak 6:9, 13
2 Akor. 12:21Aro 13:13; Aga 5:19; Aef 4:19; 2Pe 2:2; Yuda 4
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Werengani mu Baibulo la Dziko Latsopano (nwt)
  • 1
  • 2
  • 3
  • 4
  • 5
  • 6
  • 7
  • 8
  • 9
  • 10
  • 11
  • 12
  • 13
  • 14
  • 15
  • 16
  • 17
  • 18
  • 19
  • 20
  • 21
Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
2 Akorinto 12:1-21

2 Akorinto

12 Ndiyenera kudzitama. Zoona, kudzitama si kopindulitsa. Koma tiyeni tisiye kaye nkhani imeneyi, tipite ku nkhani yokhudza masomphenya+ ndi mauthenga ochokera kwa Ambuye. 2 Ndikudziwa munthu wina wogwirizana ndi Khristu. Zaka 14 zapitazo, munthu ameneyu anakwatulidwira kumwamba kwachitatu. Kaya zimenezo zinachitika ali m’thupi kapena ali kunja kwa thupi sindikudziwa. Akudziwa ndi Mulungu.+ 3 Zoonadi, ndikumudziwa munthu ameneyu. Kaya anakwatulidwa ali m’thupi kapena kunja kwa thupi,+ sindikudziwa. Akudziwa ndi Mulungu. 4 Iye anakwatulidwa n’kukalowa m’paradaiso,+ ndipo ali m’paradaisomo anamva mawu osatchulika, amene sikololeka munthu kuwanena. 5 Ndidzadzitamandira chifukwa cha munthu ameneyo, koma sindidzadzitamandira chifukwa cha ineyo, kupatulapo pa kufooka kwanga.+ 6 Ngati ndingafune kudzitamandira, si kuti ndikhala wodzikweza,+ chifukwa ndikhala ndikunena choonadi. Koma sindikudzitamandira, chifukwa ndikufuna kuti inuyo mundiyamikire pa zinthu zokhazo zimene mukuona kapena kumva kwa ine. 7 Chifukwa cha kuchuluka kwa mauthenga amene anaululidwa kwa ine, aliyense asandiganizire koposa mmene ayenera kundiganizira.

Chotero, kuti ndisadzikweze mopitirira muyezo,+ ndinapatsidwa munga m’thupi,+ mngelo wa Satana woti azindimenya nthawi zonse, kuti ndisadzikweze mopitirira muyezo. 8 Pa nkhaniyi, katatu+ konse ndinachonderera Ambuye kuti mungawu undichoke, 9 koma anandiuza motsimikiza kuti: “Kukoma mtima kwakukulu kumene ndakusonyeza n’kokukwanira,+ pakuti mphamvu yanga imakhala yokwanira iweyo ukakhala wofooka.”+ Choncho, ndidzadzitamandira mosangalala kwambiri pa kufooka kwanga,+ kuti mphamvu ya Khristu ikhalebe pamutu panga ngati hema. 10 Chotero ndimasangalala ndi kufooka, zitonzo, zosowa zanga, mazunzo ndi zovuta zina, chifukwa cha Khristu. Pakuti pamene ndili wofooka, m’pamene ndimakhala wamphamvu.+

11 Ndakhala wodzikweza tsopano. Ndinu mwandikakamiza+ kukhala wotero, popeza simunanene za zinthu zabwino zimene ndachita, ngakhale kuti munayenera kutero. Pakuti sindinachepe mwanjira ina iliyonse kwa atumwi anu apamwambawo,+ ngakhale kuti si ine kanthu m’maso mwanu.+ 12 Ndithudi inuyo munaona umboni wakuti ndine mtumwi,+ poona mmene ndinapiririra,+ komanso poona zizindikiro, zodabwitsa, ndi ntchito zamphamvu zimene ndinachita.+ 13 Kodi munakhala ochepa m’njira yotani kwa mipingo yonse? Mwina m’njira yoti ineyo sindinakhale katundu wolemetsa kwa inu.+ Chonde, ndikhululukireni cholakwa chimenechi.

14 Kanotu ndi kachitatu+ kukhala wokonzeka kubwera kwa inu, koma sindidzakhala katundu wolemetsa. Pakuti sindikufuna zinthu zanu,+ koma inuyo. Paja ana+ sayenera kusunga chuma kuti chidzathandize makolo awo m’tsogolo, koma makolo ndi amene ayenera kusungira ana awo.+ 15 Koma ineyo ndidzagwiritsa ntchito zinthu zanga zonse ndipo ndidzadzipereka ndi moyo wanga wonse chifukwa cha miyoyo yanu.+ Ngati ineyo ndimakukondani kwambiri chonchi, kodi inuyo mukuyenera kundikonda mochepa? 16 Mulimonse mmene zinakhalira, sindinakulemetseni.+ Ngakhale zili choncho, inuyo mukuti, “ndinakuchenjererani” ndi kukukolani “mwachinyengo.”+ 17 Koma sindinakuchenjerereni kudzera mwa aliyense wa anthu amene ndinawatumiza kwa inu, ndinatero ngati? 18 Tito ndinamuchonderera kuti abwere kwa inu ndipo ndinatumiza m’bale wina limodzi naye. Kodi Titoyo anakuchenjererani m’pang’ono pomwe ngati?+ Ayi ndithu sanatero. Tinayenda mumzimu umodzi,+ kodi si choncho? M’mapazi amodzimodzi, si choncho kodi?

19 Kodi nthawi yonseyi mwakhala mukuganiza kuti tikudzitchinjiriza pamaso panu? Tikulankhula pamaso pa Mulungu mogwirizana ndi Khristu. Komatu okondedwa, tikuchita zonse kuti tikulimbikitseni.+ 20 Ndikuopa kuti mwinamwake ndikadzafika,+ sindidzakupezani mmene ndikanafunira. Kwa inunso sindidzakhala mmene mukanafunira. M’malomwake, ndidzapeza ndewu, nsanje,+ kukwiyitsana, mikangano, miseche, manong’onong’o, kudzitukumula, ndi zisokonezo.+ 21 Mwina ndikadzabweranso, Mulungu wanga adzandichititsa manyazi pakati panu. Ndipo mwina ndidzalirira anthu ambiri amene anachimwa+ koma sanalape pa zonyansa zawo, dama*+ lawo, ndi khalidwe lawo lotayirira+ limene akhala akuchita.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena