1 Mbiri 1:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Patapita nthawi, Baala-hanani anamwalira ndipo Hadadi anayamba kulamulira m’malo mwake. Dzina la mzinda wake linali Pau, ndipo mkazi wake dzina lake linali Mehetabele mwana wa Matiredi mwana wamkazi wa Mezahabu.+
50 Patapita nthawi, Baala-hanani anamwalira ndipo Hadadi anayamba kulamulira m’malo mwake. Dzina la mzinda wake linali Pau, ndipo mkazi wake dzina lake linali Mehetabele mwana wa Matiredi mwana wamkazi wa Mezahabu.+