-
Machitidwe 14:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Koma atumwiwo, Baranaba ndi Paulo, atamva zimenezi anang’amba malaya awo akunja ndi kuthamanga kukalowa m’khamu la anthu lija akufuula
-