Numeri 16:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Anthuwo atamva zimenezi anagwada n’kuwerama mpaka nkhope zawo pansi, n’kunena kuti: “Chonde Mulungu, inu Mulungu amene amapereka moyo kwa zamoyo zonse,+ kodi kuchimwa kwa munthu mmodzi yekha n’kumene mungapsere mtima khamu lonseli?”+ Numeri 20:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pamenepo Mose ndi Aroni anachoka pamaso pa mpingowo n’kupita kukhomo la chihema chokumanako. Kumeneko, anagwada n’kuwerama mpaka nkhope zawo pansi,+ ndipo ulemerero wa Yehova unayamba kuonekera kwa iwo.+
22 Anthuwo atamva zimenezi anagwada n’kuwerama mpaka nkhope zawo pansi, n’kunena kuti: “Chonde Mulungu, inu Mulungu amene amapereka moyo kwa zamoyo zonse,+ kodi kuchimwa kwa munthu mmodzi yekha n’kumene mungapsere mtima khamu lonseli?”+
6 Pamenepo Mose ndi Aroni anachoka pamaso pa mpingowo n’kupita kukhomo la chihema chokumanako. Kumeneko, anagwada n’kuwerama mpaka nkhope zawo pansi,+ ndipo ulemerero wa Yehova unayamba kuonekera kwa iwo.+