Genesis 43:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Tirigu amene anachokera naye ku Iguputo uja atatha,+ bambo awo anawauza kuti: “Pitaninso mukatigulireko chakudya pang’ono.”+
2 Tirigu amene anachokera naye ku Iguputo uja atatha,+ bambo awo anawauza kuti: “Pitaninso mukatigulireko chakudya pang’ono.”+