Genesis 29:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma Yakobo anakonda Rakele, ndiye anati: “Ndine wokonzeka kukugwirirani ntchito zaka 7, kuti mudzandipatse Rakele mwana wanu wamng’onoyu.”+ Genesis 30:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Rakele anakhala ndi pakati n’kubereka mwana wamwamuna. Ndiyeno iye anati: “Mulungu wandichotsera chitonzo.”+ Genesis 35:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pomalizira pake, pamene moyo wake+ unali kutayika (pakuti anamwalira),+ anatcha mwanayo dzina lakuti Beni-oni.* Koma bambo ake anamutcha Benjamini.*+ Genesis 46:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ana a Rakele,+ mkazi wa Yakobo, anali Yosefe+ ndi Benjamini.+
18 Koma Yakobo anakonda Rakele, ndiye anati: “Ndine wokonzeka kukugwirirani ntchito zaka 7, kuti mudzandipatse Rakele mwana wanu wamng’onoyu.”+
23 Rakele anakhala ndi pakati n’kubereka mwana wamwamuna. Ndiyeno iye anati: “Mulungu wandichotsera chitonzo.”+
18 Pomalizira pake, pamene moyo wake+ unali kutayika (pakuti anamwalira),+ anatcha mwanayo dzina lakuti Beni-oni.* Koma bambo ake anamutcha Benjamini.*+