Genesis 45:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Inuyo, ana anu, adzukulu anu, nkhosa ndi ng’ombe zanu, ndi zonse zimene muli nazo mudzakhale m’dziko la Goseni+ pafupi ndi ine. Ekisodo 8:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pa tsiku limenelo ndidzapatula dera la Goseni kumene kuli anthu anga, kuti kusakhale tizilombo toyamwa magazi.+ Ndidzatero kuti udziwe kuti ine ndine Yehova, ndipo ndili ndi mphamvu padziko lonse lapansi.+
10 Inuyo, ana anu, adzukulu anu, nkhosa ndi ng’ombe zanu, ndi zonse zimene muli nazo mudzakhale m’dziko la Goseni+ pafupi ndi ine.
22 Pa tsiku limenelo ndidzapatula dera la Goseni kumene kuli anthu anga, kuti kusakhale tizilombo toyamwa magazi.+ Ndidzatero kuti udziwe kuti ine ndine Yehova, ndipo ndili ndi mphamvu padziko lonse lapansi.+