Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 7:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Pamenepo Aiguputo adzadziwa kuti ine ndine Yehova ndikadzatambasula dzanja langa ndi kukantha Iguputo.+ Motero ndidzatulutsa ana a Isiraeli m’dzikolo.”+

  • Ekisodo 8:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Pamenepo Farao anayankha kuti: “Mawa.” Ndiyeno Mose anati: “Zidzachitika monga mwa mawu anu, kuti mudziwe kuti palibenso wina wofanana ndi Yehova Mulungu wathu,+

  • 1 Samueli 17:46
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 46 Lero Yehova akupereka m’manja mwanga,+ ndipo ndikupha ndi kukudula mutu. Lero ndipereka mitembo ya anthu a m’misasa ya Afilisiti kwa mbalame zam’mlengalenga ndi kwa zilombo zakutchire.+ Anthu onse a padziko lapansi adzadziwa kuti Isiraeli ali ndi Mulungu.+

  • 1 Mafumu 20:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Kenako munthu wa Mulungu woona+ uja anapita kwa mfumu ya Isiraeli n’kuiuza kuti: “Yehova wanena kuti, ‘Popeza Asiriya anena kuti: “Yehova ndi Mulungu wa mapiri, osati Mulungu wa zigwa,” ndipereka khamu lalikulu lonseli m’manja mwako,+ ndipo anthu inu mudziwadi kuti ine ndine Yehova.’”+

  • 2 Mafumu 19:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Tsopano inu Yehova Mulungu wathu,+ chonde tipulumutseni+ m’manja mwake, kuti maufumu onse a padziko lapansi adziwe kuti inu Yehova, inu nokha ndiye Mulungu.”+

  • Ezekieli 34:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 ‘Iwo adzadziwa kuti ine, Yehova Mulungu wawo, ndili nawo limodzi+ ndiponso kuti iwowo, a nyumba ya Isiraeli ndi anthu anga,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena