Miyambo 12:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Wolima nthaka yake adzakhala ndi chakudya chokwanira,+ koma wofunafuna zinthu zopanda pake ndi wopanda nzeru mumtima mwake.+ 1 Timoteyo 5:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pakuti lemba limati: “Usamange ng’ombe pakamwa pamene ikupuntha mbewu.”+ Komanso limati: “Wantchito ayenera kulandira malipiro ake.”+
11 Wolima nthaka yake adzakhala ndi chakudya chokwanira,+ koma wofunafuna zinthu zopanda pake ndi wopanda nzeru mumtima mwake.+
18 Pakuti lemba limati: “Usamange ng’ombe pakamwa pamene ikupuntha mbewu.”+ Komanso limati: “Wantchito ayenera kulandira malipiro ake.”+