Ekisodo 19:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tsopano ngati mudzalabadiradi+ mawu anga ndi kusunga pangano langa,+ pamenepo mudzakhaladi chuma changa chapadera pakati pa anthu ena onse,+ chifukwa dziko lonse lapansi ndi langa.+ Deuteronomo 30:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Koma iwe udzatembenuka ndi kumvera mawu a Yehova ndi kutsatira malamulo ake onse amene ndikukupatsa lero.+
5 Tsopano ngati mudzalabadiradi+ mawu anga ndi kusunga pangano langa,+ pamenepo mudzakhaladi chuma changa chapadera pakati pa anthu ena onse,+ chifukwa dziko lonse lapansi ndi langa.+
8 “Koma iwe udzatembenuka ndi kumvera mawu a Yehova ndi kutsatira malamulo ake onse amene ndikukupatsa lero.+