Genesis 12:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Odalitsa iwe ndidzawadalitsa, ndipo otemberera iwe ndidzawatemberera.+ Mabanja onse a padziko lapansi adzapeza madalitso* chifukwa cha iwe.”+ Deuteronomo 30:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndipo Yehova Mulungu wanu adzaikadi matemberero onsewa pa adani anu, ndi onse odana ndi inu amene anakuzunzani.+
3 Odalitsa iwe ndidzawadalitsa, ndipo otemberera iwe ndidzawatemberera.+ Mabanja onse a padziko lapansi adzapeza madalitso* chifukwa cha iwe.”+
7 Ndipo Yehova Mulungu wanu adzaikadi matemberero onsewa pa adani anu, ndi onse odana ndi inu amene anakuzunzani.+