Deuteronomo 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Yehova adzakuchotserani matenda onse. Ndipo sadzakugwetserani matenda onse oipa a ku Iguputo amene inu mukuwadziwa,+ koma adzawagwetsera pa onse odana nanu. Salimo 103:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tamanda amene akukukhululukira zolakwa zako zonse,+Iye amene akukuchiritsa matenda ako onse.+
15 Yehova adzakuchotserani matenda onse. Ndipo sadzakugwetserani matenda onse oipa a ku Iguputo amene inu mukuwadziwa,+ koma adzawagwetsera pa onse odana nanu.