Ekisodo 20:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Uzilemekeza bambo ako ndi mayi ako+ kuti masiku ako atalike m’dziko limene Yehova Mulungu wako akukupatsa.+ Salimo 92:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Zinthu zidzapitiriza kuwayendera bwino ngakhale atachita imvi,+Adzakhalabe onenepa ndi athanzi,+
12 “Uzilemekeza bambo ako ndi mayi ako+ kuti masiku ako atalike m’dziko limene Yehova Mulungu wako akukupatsa.+