Deuteronomo 7:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Yehova Mulungu wako adzawaperekadi kwa iwe ndi kuwabalalitsa atasokonezeka kwambiri, kufikira atawonongedwa.+
23 Yehova Mulungu wako adzawaperekadi kwa iwe ndi kuwabalalitsa atasokonezeka kwambiri, kufikira atawonongedwa.+