-
Ekisodo 38:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Ndipo siliva wa anthu amene anawerengedwa m’khamu la Isiraeli, anali matalente 100 ndi masekeli 1,775 pamuyezo wolingana ndi sekeli la kumalo oyera.
-