Ekisodo 36:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndiyeno anapanga mafelemu awiri kuti akhale mizati ya m’makona akumbuyo a chihema chopatulika.+