Ekisodo 26:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndiyeno upange mafelemu awiri kuti akhale ochirikiza m’makona akumbuyo a chihema chopatulika.+