Ekisodo 36:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 ndi mipiringidzo inanso isanu yogwira mafelemu a mbali ina ya chihema chopatulika. Anapanganso mipiringidzo ina isanu yogwira mafelemu a kumbuyo kwa chihema chopatulika, chakumadzulo.+
32 ndi mipiringidzo inanso isanu yogwira mafelemu a mbali ina ya chihema chopatulika. Anapanganso mipiringidzo ina isanu yogwira mafelemu a kumbuyo kwa chihema chopatulika, chakumadzulo.+