Ekisodo 26:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Mipiringidzo isanu yogwira mafelemu a mbali ina ya chihema chopatulika, mipiringidzo inanso isanu yogwira mafelemu akumbuyo kwa chihema chopatulika, chakumadzulo.+
27 Mipiringidzo isanu yogwira mafelemu a mbali ina ya chihema chopatulika, mipiringidzo inanso isanu yogwira mafelemu akumbuyo kwa chihema chopatulika, chakumadzulo.+