Ekisodo 38:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Ndiyeno anapanga guwa lansembe zopsereza la matabwa a mthethe, m’litali mwake mikono isanu, ndipo m’lifupi mikono isanu. Guwalo linali lofanana muyezo wake mbali zake zonse zinayi, ndipo msinkhu wake linali mikono itatu.+ Ekisodo 40:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ndiyeno anaika guwa lansembe+ zopsereza pakhomo la chihema chopatulika, kapena kuti chihema chokumanako, kuti aziperekerapo nsembe yopsereza+ ndi nsembe yambewu, monga mmene Yehova analamulira Mose. 2 Mbiri 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno anapanga guwa lansembe lamkuwa.+ Guwalo linali lalikulu mikono 20 m’litali, mikono 20 m’lifupi ndipo kuchokera pansi kufika pamwamba linali lalitali mikono 10.+ Aheberi 13:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ife tili ndi guwa lansembe limene ochita utumiki wopatulika kuchihema, alibe ulamuliro wodya za paguwapo.+
38 Ndiyeno anapanga guwa lansembe zopsereza la matabwa a mthethe, m’litali mwake mikono isanu, ndipo m’lifupi mikono isanu. Guwalo linali lofanana muyezo wake mbali zake zonse zinayi, ndipo msinkhu wake linali mikono itatu.+
29 Ndiyeno anaika guwa lansembe+ zopsereza pakhomo la chihema chopatulika, kapena kuti chihema chokumanako, kuti aziperekerapo nsembe yopsereza+ ndi nsembe yambewu, monga mmene Yehova analamulira Mose.
4 Ndiyeno anapanga guwa lansembe lamkuwa.+ Guwalo linali lalikulu mikono 20 m’litali, mikono 20 m’lifupi ndipo kuchokera pansi kufika pamwamba linali lalitali mikono 10.+
10 Ife tili ndi guwa lansembe limene ochita utumiki wopatulika kuchihema, alibe ulamuliro wodya za paguwapo.+