Ekisodo 35:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 guwa lansembe+ zopsereza ndi sefa wake wa zitsulo zamkuwa zolukanalukana, mitengo yake yonyamulira ndi zipangizo zake zonse, beseni+ ndi choikapo chake.
16 guwa lansembe+ zopsereza ndi sefa wake wa zitsulo zamkuwa zolukanalukana, mitengo yake yonyamulira ndi zipangizo zake zonse, beseni+ ndi choikapo chake.