27 Ndiyeno munthu wa Mulungu+ anapita kwa Eli ndi kumuuza kuti: “Yehova wanena kuti, ‘Kodi ine sindinadzisonyeze kunyumba ya kholo lako pamene anali akapolo kunyumba ya Farao ku Iguputo?+
32 ‘Ine ndine Mulungu wa makolo ako. Ndine Mulungu wa Abulahamu, wa Isaki ndi wa Yakobo.’+ Ponjenjemera ndi mantha, Mose sanathenso kupitiriza kuyang’anitsitsa chitsambacho.