Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 6:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Koma Mose anayankha Yehova kuti: “Komatu ana a Isiraeli sanandimvere,+ nanga Farao akandimvera bwanji?+ Pakuti ndimalankhula movutikira.”*+

  • Numeri 12:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Moseyo anali munthu wofatsa kwambiri+ kuposa anthu onse amene anali padziko lapansi.

  • Yeremiya 1:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Koma ine ndinati: “Haa! Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, ine sindingathe kulankhula+ chifukwa ndine mwana.”+

  • Machitidwe 7:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Chotero Mose anaphunzira nzeru+ zonse za Aiguputo. Ndipo anali wamphamvu m’mawu+ ndi m’zochita zake.

  • 2 Akorinto 11:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Ngati ndilibe luso la kulankhula,+ si kuti ndine wosadziwanso zinthu.+ Koma m’njira iliyonse tinakusonyezani kuti ndife odziwa zinthu pa zonse.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena