Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Akorinto 11
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

2 Akorinto 11:1

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +2Ak 5:13

2 Akorinto 11:2

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Afi 1:8
  • +Chv 21:2, 9; 22:17
  • +Mko 2:19
  • +Le 21:13; Aef 5:23
  • +Aef 5:27; Akl 1:28

2 Akorinto 11:3

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Ge 3:4; 1Ti 2:14
  • +Yoh 8:44; 1Ti 6:5; Ahe 13:9; 2Pe 3:17; 2Yo 8
  • +1Ak 6:15

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    ‘Mulungu Apitirize Kukukondani’, tsa. 192

    Nsanja ya Olonda,

    10/15/2002, tsa. 8

    2/15/1987, ptsa. 11-12

2 Akorinto 11:4

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aga 1:7
  • +1Yo 4:3
  • +Aga 1:8
  • +Afi 2:21; 2Yo 10

2 Akorinto 11:5

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Ak 15:10; 2Ak 11:23
  • +2Ak 12:11; Aga 2:6

2 Akorinto 11:6

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Eks 4:10; 2Ak 10:10
  • +1Ak 2:13
  • +Aef 3:4

2 Akorinto 11:7

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Ak 2:3; 2Ak 10:1
  • +Mac 18:3; 1Ak 9:18

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 148-150

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    4/2019, tsa. 4

2 Akorinto 11:8

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Afi 4:10

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    12/1/1989, ptsa. 25-26

2 Akorinto 11:9

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +2Ak 12:13
  • +Afi 4:15
  • +1At 2:9

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 151

    Nsanja ya Olonda,

    6/15/1990, ptsa. 18-19

    12/1/1989, ptsa. 25-26

2 Akorinto 11:10

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aro 9:1
  • +1Ak 9:15

2 Akorinto 11:11

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +2Ak 6:11; 7:3; 12:15

2 Akorinto 11:12

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Ak 9:12

2 Akorinto 11:13

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Sl 101:7; 119:118; Mac 5:3; Aef 4:14
  • +Aro 16:18; 2Ak 2:17; 2Pe 2:1

2 Akorinto 11:14

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aga 1:8; 2At 2:9

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    2/15/2004, ptsa. 4-5

    3/1/2002, tsa. 11

    2/15/1987, tsa. 11

2 Akorinto 11:15

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yoh 8:44
  • +Mt 16:27; Aro 2:6; Aga 5:10; Afi 3:19; 2Ti 4:14

2 Akorinto 11:16

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +2Ak 10:8

2 Akorinto 11:17

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Ak 3:21

2 Akorinto 11:18

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Afi 3:4

2 Akorinto 11:20

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aga 2:4; 4:9; 5:1
  • +Afi 3:19

2 Akorinto 11:21

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +2Ak 5:13; 12:11

2 Akorinto 11:22

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 22:3
  • +Aro 11:1; Afi 3:5

2 Akorinto 11:23

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +2Ak 11:5
  • +Aro 11:13; 1Ak 15:10
  • +Mac 16:24
  • +Mac 9:16; 2Ak 6:4; 1Pe 2:21

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    10/2021, tsa. 26

    Nsanja ya Olonda,

    7/15/2000, ptsa. 26-27

2 Akorinto 11:24

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +De 25:3

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    7/15/2000, ptsa. 26-27

2 Akorinto 11:25

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 16:22
  • +Mac 14:19
  • +Mac 27:41

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    7/15/2000, ptsa. 26-27

    6/15/1990, ptsa. 12, 16

2 Akorinto 11:26

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 20:3
  • +Mac 23:10
  • +Mac 14:5
  • +Mac 13:50

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    7/15/2000, ptsa. 26-27

    9/1/1992, tsa. 12

    6/15/1990, ptsa. 11, 24-25

2 Akorinto 11:27

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 20:31
  • +1Ak 4:11
  • +2Ak 6:5

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    7/15/2000, ptsa. 26-27

2 Akorinto 11:28

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +2Ak 2:4; Akl 2:1

2 Akorinto 11:29

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Ak 9:22

2 Akorinto 11:30

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +2Ak 12:5

2 Akorinto 11:32

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 9:24

2 Akorinto 11:33

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 9:25

Mabaibulo Ena

Dinani pa nambala ya vesi kuti muone mavesi a m'Baibulo lina ofanana ndi vesilo.

Malemba Ena

2 Akor. 11:12Ak 5:13
2 Akor. 11:2Afi 1:8
2 Akor. 11:2Chv 21:2, 9; 22:17
2 Akor. 11:2Mko 2:19
2 Akor. 11:2Le 21:13; Aef 5:23
2 Akor. 11:2Aef 5:27; Akl 1:28
2 Akor. 11:3Ge 3:4; 1Ti 2:14
2 Akor. 11:3Yoh 8:44; 1Ti 6:5; Ahe 13:9; 2Pe 3:17; 2Yo 8
2 Akor. 11:31Ak 6:15
2 Akor. 11:4Aga 1:7
2 Akor. 11:41Yo 4:3
2 Akor. 11:4Aga 1:8
2 Akor. 11:4Afi 2:21; 2Yo 10
2 Akor. 11:51Ak 15:10; 2Ak 11:23
2 Akor. 11:52Ak 12:11; Aga 2:6
2 Akor. 11:6Eks 4:10; 2Ak 10:10
2 Akor. 11:61Ak 2:13
2 Akor. 11:6Aef 3:4
2 Akor. 11:71Ak 2:3; 2Ak 10:1
2 Akor. 11:7Mac 18:3; 1Ak 9:18
2 Akor. 11:8Afi 4:10
2 Akor. 11:92Ak 12:13
2 Akor. 11:9Afi 4:15
2 Akor. 11:91At 2:9
2 Akor. 11:10Aro 9:1
2 Akor. 11:101Ak 9:15
2 Akor. 11:112Ak 6:11; 7:3; 12:15
2 Akor. 11:121Ak 9:12
2 Akor. 11:13Sl 101:7; 119:118; Mac 5:3; Aef 4:14
2 Akor. 11:13Aro 16:18; 2Ak 2:17; 2Pe 2:1
2 Akor. 11:14Aga 1:8; 2At 2:9
2 Akor. 11:15Yoh 8:44
2 Akor. 11:15Mt 16:27; Aro 2:6; Aga 5:10; Afi 3:19; 2Ti 4:14
2 Akor. 11:162Ak 10:8
2 Akor. 11:171Ak 3:21
2 Akor. 11:18Afi 3:4
2 Akor. 11:20Aga 2:4; 4:9; 5:1
2 Akor. 11:20Afi 3:19
2 Akor. 11:212Ak 5:13; 12:11
2 Akor. 11:22Mac 22:3
2 Akor. 11:22Aro 11:1; Afi 3:5
2 Akor. 11:232Ak 11:5
2 Akor. 11:23Aro 11:13; 1Ak 15:10
2 Akor. 11:23Mac 16:24
2 Akor. 11:23Mac 9:16; 2Ak 6:4; 1Pe 2:21
2 Akor. 11:24De 25:3
2 Akor. 11:25Mac 16:22
2 Akor. 11:25Mac 14:19
2 Akor. 11:25Mac 27:41
2 Akor. 11:26Mac 20:3
2 Akor. 11:26Mac 23:10
2 Akor. 11:26Mac 14:5
2 Akor. 11:26Mac 13:50
2 Akor. 11:27Mac 20:31
2 Akor. 11:271Ak 4:11
2 Akor. 11:272Ak 6:5
2 Akor. 11:282Ak 2:4; Akl 2:1
2 Akor. 11:291Ak 9:22
2 Akor. 11:302Ak 12:5
2 Akor. 11:32Mac 9:24
2 Akor. 11:33Mac 9:25
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Werengani mu Baibulo la Dziko Latsopano (nwt)
  • 1
  • 2
  • 3
  • 4
  • 5
  • 6
  • 7
  • 8
  • 9
  • 10
  • 11
  • 12
  • 13
  • 14
  • 15
  • 16
  • 17
  • 18
  • 19
  • 20
  • 21
  • 22
  • 23
  • 24
  • 25
  • 26
  • 27
  • 28
  • 29
  • 30
  • 31
  • 32
  • 33
Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
2 Akorinto 11:1-33

2 Akorinto

11 Ndikanakonda kuti mundilole kuti ndidzikweze pang’ono.+ Ndipotu zoona zake n’zakuti, mwandilola kale. 2 Ndikukuchitirani nsanje,+ ngati imene Mulungu amakuchitirani, popeza ndine ndinakuchititsani kulonjezedwa ukwati+ ndi mwamuna mmodzi,+ Khristu,+ ndipo ndikufuna kukuperekani ngati namwali woyera+ kwa iye. 3 Koma nkhawa yanga ndi yakuti mwina, monga mmene njoka inanamizira Hava+ ndi chinyengo chake, maganizo anunso angapotozedwe+ kuti musakhalenso oona mtima ndi oyera ngati mmene muyenera kuchitira kwa Khristu.+ 4 Chifukwa panopa wina akabwera kwa inu n’kulalikira za Yesu wosiyana ndi amene tinamulalikira,+ kapena wina akakubweretserani mzimu wosiyana ndi umene munalandira kale,+ kapena uthenga wabwino+ wosiyana ndi umene munaulandira, inu mumangomulolera munthu woteroyo.+ 5 Koma ine ndikuona kuti sindikuchepa+ mwanjira ina iliyonse kwa atumwi anu apamwambawo.+ 6 Ngati ndilibe luso la kulankhula,+ si kuti ndine wosadziwanso zinthu.+ Koma m’njira iliyonse tinakusonyezani kuti ndife odziwa zinthu pa zonse.+

7 Kapena kodi ndinachita tchimo pamene ndinadzichepetsa+ kuti inuyo mukwezedwe, muja ndinalengeza mosangalala uthenga wabwino wa Mulungu kwa inu, popanda inuyo kutayirapo ndalama?+ 8 Ndinalanda mipingo ina zinthu zawo polandira chithandizo chawo kuti nditumikire inuyo.+ 9 Koma pamene ndinasowa zofunika zina ndili kwanuko, sindinalemetse ngakhale munthu mmodzi,+ popeza abale amene anachokera ku Makedoniya+ anandipatsa zonse zimene ndinali kuzisowa. Ndithu, sindinakulemetseni m’njira iliyonse, ndipo ndipitirizabe kutero.+ 10 Ndikulankhula choonadi+ cha Khristu, choncho palibe angandiletse kudzitamandira+ m’madera a ku Akaya. 11 Kodi ndachita zimenezi chifukwa chiyani? Chifukwa sindikukondani? Mulungu akudziwa kuti ndimakukondani.+

12 Tsopano ndipitiriza kuchita zimene ndikuchita,+ kuti nditsekereze anthu amene akuyesayesa kupeza chifukwa choti anamizire kuti ndi ofanana ndi ife, podzitamandira chifukwa cha udindo wawo. 13 Pakuti amuna oterowo ndi atumwi onama, antchito achinyengo,+ odzisandutsa atumwi a Khristu.+ 14 Ndipo zimenezo n’zosadabwitsa, popeza ngakhale Satana amadzisandutsa mngelo wa kuwala.+ 15 Choncho n’zosadabwitsa ngati atumiki ake+ nawonso amadzisandutsa atumiki a chilungamo. Koma mapeto awo adzakhala monga mwa ntchito zawo.+

16 Ndikubwerezanso kunena kuti, munthu asandiyese wodzikweza. Koma ngati mukundionabe motero, ndilandirenibe monga wodzikweza yemweyo, kuti nanenso ndidzitame pang’ono.+ 17 Zimene ndikulankhulazi, ndikulankhula ngati mmene amalankhulira anthu odzitama ndiponso odzidalira kwambiri. Sindikulankhula motsatira chitsanzo cha Ambuye ayi, koma ngati mmene amalankhulira anthu opanda nzeru.+ 18 Popeza anthu ambiri akudzitama pa zinthu za m’dzikoli,+ inenso ndidzitama. 19 Pakuti mumalolera mosangalala anthu odzikweza, chifukwa mumadziona kuti ndinu ololera. 20 Ndipo mumalolera aliyense wokumangani ukapolo,+ womeza zimene muli nazo, wokulandani zimene muli nazo, wodzikweza pa inu, ndiponso aliyense wokuwombani mbama.+

21 Ndikunena zimenezi mopeputsa ifeyo, ngati kuti ndife ofooka.

Koma ngati wina aliyense akuchita chinachake molimba mtima, ndikulankhula ngati wodzitama,+ inenso ndikuchita chinthu chomwecho molimba mtima. 22 Kodi iwo ndi Aheberi? Inenso ndine Mheberi.+ Kodi ndi Aisiraeli? Inenso ndine Mwisiraeli. Kapena iwo ndi mbewu ya Abulahamu? Inenso chimodzimodzi.+ 23 Ndi atumiki a Khristu kapena? Ndikuyankha ngati wamisala, ineyo ndiye weniweni woposanso iwowo:+ m’ntchito zovuta mowirikiza koposa,+ m’ndende osachita kunena,+ kumenyedwa kosawerengeka, kutsala pang’ono kufa kawirikawiri.+ 24 Kasanu Ayuda anandikwapula zikoti 40+ kuchotsera chimodzi. 25 Katatu anandimenya ndi ndodo.+ Kamodzi anandiponya miyala.+ Chombo chinandiswekerapo katatu.+ Kamodzi ndinakhala pamadzi akuya usiku ndi usana wonse. 26 Pa maulendo kawirikawiri, zoopsa za m’mitsinje, zoopsa za achifwamba pamsewu,+ zoopsa zochokera kwa anthu a mtundu wanga,+ zoopsa zochokera kwa anthu a mitundu ina,+ zoopsa mumzinda,+ zoopsa m’chipululu, zoopsa za panyanja, zoopsa pakati pa abale onyenga, 27 m’ntchito yolimba ndi m’thukuta, kawirikawiri osagona tulo usiku,+ njala ndi ludzu,+ nthawi zambiri osadya chakudya,+ kuzizidwa ndi kukhala wosavala.

28 Kuwonjezera pa zinthu za kunja kwa thupi zimenezo, palinso chimene chimandivutitsa maganizo tsiku ndi tsiku, ndicho nkhawa imene ndimakhala nayo pa mipingo yonse.+ 29 Ndani ali wofooka,+ ine osakhalanso wofooka? Ndani wakhumudwitsidwa, ine osakwiya nazo?

30 Ngati ndiyenera kudzitama, ndidzadzitama+ pa zinthu zokhudza kufooka kwanga. 31 Mulungu ndi Atate wa Ambuye Yesu, amene ali woyenera kutamandidwa kwamuyaya, akudziwa kuti sindikunama. 32 Ku Damasiko, bwanamkubwa wa mfumu Areta anali kulondera mzinda wa Adamasiko kuti andigwire,+ 33 koma ndinaikidwa m’dengu n’kutsitsidwa pawindo la mpanda wa mzindawo,+ ndipo ndinapulumuka m’manja mwake.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena