Ekisodo 29:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Ndiyeno kunkhosayo utengeko mafuta ndi mchira wa mafuta+ ndi mafuta okuta matumbo, mafuta a pachiwindi, impso ziwiri ndi mafuta ake ndi mwendo wakumbuyo wa kudzanja lamanja,+ pakuti nkhosayo ndi yowalongera unsembe.+ Levitiko 7:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Limeneli ndilo lamulo lokhudza nsembe yopsereza,+ nsembe yambewu,+ nsembe yamachimo,+ nsembe ya kupalamula,+ nyama yoperekedwa polonga munthu unsembe+ ndiponso nsembe yachiyanjano,+
22 “Ndiyeno kunkhosayo utengeko mafuta ndi mchira wa mafuta+ ndi mafuta okuta matumbo, mafuta a pachiwindi, impso ziwiri ndi mafuta ake ndi mwendo wakumbuyo wa kudzanja lamanja,+ pakuti nkhosayo ndi yowalongera unsembe.+
37 Limeneli ndilo lamulo lokhudza nsembe yopsereza,+ nsembe yambewu,+ nsembe yamachimo,+ nsembe ya kupalamula,+ nyama yoperekedwa polonga munthu unsembe+ ndiponso nsembe yachiyanjano,+