15 Iwo azibweretsa mwendo wa gawo lopatulika ndi nganga ya nsembe yoweyula,+ pamodzi ndi mafuta a nsembe zotentha ndi moto, kuti woperekayo aziweyule uku ndi uku pamaso pa Yehova. Zimenezi zizikhala gawo lanu+ ndi gawo la ana anu mpaka kalekale, monga mmene Yehova walamulira.”