Levitiko 8:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Kenako Mose anatenga nganga+ ndi kuiweyula uku ndi uku monga nsembe yoweyula yoperekedwa kwa Yehova.+ Nganga imeneyi anaitenga pa nkhosa yowalongera unsembe ndipo inakhala gawo+ la Mose, monga mmene Yehova analamulira Mose. Numeri 18:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Uzitenga nyama yake kuti ikhale yako, mofanana ndi nganga ya nsembe yoweyula, komanso mwendo wam’mbuyo wakumanja.+
29 Kenako Mose anatenga nganga+ ndi kuiweyula uku ndi uku monga nsembe yoweyula yoperekedwa kwa Yehova.+ Nganga imeneyi anaitenga pa nkhosa yowalongera unsembe ndipo inakhala gawo+ la Mose, monga mmene Yehova analamulira Mose.
18 Uzitenga nyama yake kuti ikhale yako, mofanana ndi nganga ya nsembe yoweyula, komanso mwendo wam’mbuyo wakumanja.+