Ekisodo 28:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Ndipo uveke Aroni m’bale wako pamodzi ndi ana ake zinthu zimenezi. Ukatero uwadzoze,+ uwapatse mphamvu*+ ndi kuwayeretsa, ndipo atumikire monga ansembe anga. Levitiko 8:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Musachoke pakhomo la chihema chokumanako kwa masiku 7,+ kufikira tsiku lomaliza la kulongedwa kwanu unsembe, chifukwa kukupatsani mphamvu* kudzatenga masiku 7.+ 2 Akorinto 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Sitinganene kuti ndife oyenera kugwira ntchito imeneyi chifukwa cha mphamvu zathu,+ koma ndife oyenera kugwira ntchito imeneyi chifukwa cha Mulungu,+
41 Ndipo uveke Aroni m’bale wako pamodzi ndi ana ake zinthu zimenezi. Ukatero uwadzoze,+ uwapatse mphamvu*+ ndi kuwayeretsa, ndipo atumikire monga ansembe anga.
33 Musachoke pakhomo la chihema chokumanako kwa masiku 7,+ kufikira tsiku lomaliza la kulongedwa kwanu unsembe, chifukwa kukupatsani mphamvu* kudzatenga masiku 7.+
5 Sitinganene kuti ndife oyenera kugwira ntchito imeneyi chifukwa cha mphamvu zathu,+ koma ndife oyenera kugwira ntchito imeneyi chifukwa cha Mulungu,+