Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 51:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Inu Yehova, tsegulani milomo yangayi,+

      Kuti pakamwa panga patamande inu.+

  • Salimo 143:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ndiphunzitseni kuchita chifuniro chanu,+

      Pakuti inu ndinu Mulungu wanga.+

      Mzimu wanu ndi wabwino.+

      Unditsogolere m’dziko la olungama.+

  • Yesaya 50:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wandipatsa lilime la anthu ophunzitsidwa bwino+ kuti ndidziwe mmene ndingamuyankhire munthu wotopa.+ Iye amandidzutsa m’mawa uliwonse. Amandidzutsa kuti makutu anga amve ngati anthu ophunzitsidwa bwino.+

  • Maliko 13:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Koma pamene akupita nanu kukakuperekani, musafulumire kuda nkhawa kuti mukanena chiyani.+ Zimene mukapatsidwe mu ola lomwelo, mukanene zimenezo, pakuti wolankhula si inu, koma mzimu woyera.+

  • Luka 12:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Pakuti mzimu woyera+ udzakuphunzitsani mu ola lomwelo zoyenera kunena.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena