Ekisodo 25:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ine ndidzaonekera kwa iwe pamenepo ndi kulankhula nawe kuchokera pamwamba pa chivundikiro,+ pakati pa akerubi awiriwo amene ali pamwamba pa likasa la umboni. Kuchokera pamenepo ndidzakulamula zonse zokhudza ana a Isiraeli.+ Levitiko 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Tsopano kuchokera m’chihema chokumanako,+ Yehova anaitana Mose ndi kulankhula naye kuti: Numeri 17:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndodozo uziike m’chihema chokumanako, patsogolo pa Umboni,+ pamene ndimakumana nawe nthawi zonse.+
22 Ine ndidzaonekera kwa iwe pamenepo ndi kulankhula nawe kuchokera pamwamba pa chivundikiro,+ pakati pa akerubi awiriwo amene ali pamwamba pa likasa la umboni. Kuchokera pamenepo ndidzakulamula zonse zokhudza ana a Isiraeli.+