Ekisodo 40:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Pamenepo mtambo+ unayamba kuphimba chihema chokumanako, ndipo ulemerero wa Yehova unadzaza m’chihemacho. Numeri 12:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tsopano Yehova anatsika mumtambo woima njo ngati chipilala+ n’kuima pakhomo la chihema chokumanako, ndipo anaitana Aroni ndi Miriamu. Pamenepo iwo anayandikira kumeneko. 1 Mafumu 8:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chifukwa cha mtambowo, ansembewo+ analephera kupitiriza kutumikira,+ popeza ulemerero+ wa Yehova unadzaza nyumba ya Yehovayo.+
34 Pamenepo mtambo+ unayamba kuphimba chihema chokumanako, ndipo ulemerero wa Yehova unadzaza m’chihemacho.
5 Tsopano Yehova anatsika mumtambo woima njo ngati chipilala+ n’kuima pakhomo la chihema chokumanako, ndipo anaitana Aroni ndi Miriamu. Pamenepo iwo anayandikira kumeneko.
11 Chifukwa cha mtambowo, ansembewo+ analephera kupitiriza kutumikira,+ popeza ulemerero+ wa Yehova unadzaza nyumba ya Yehovayo.+