Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 16:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Pamenepo Yehova anauza Mose kuti: “Uza Aroni m’bale wako, kuti asamalowe konse m’malo oyera+ kuseri kwa nsalu yotchinga,+ patsogolo pa chivundikiro cha Likasa, kuopera kuti angafe,+ chifukwa ine ndidzaonekera mu mtambo+ pamwamba pa chivundikirocho.+

  • Numeri 9:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Pa tsiku lomanga chihema chopatulika,+ mtambo unaima pamwamba pa chihema cha Umbonicho.+ Koma kuyambira madzulo mpaka m’mawa, moto+ unali kuoneka pamwamba pa chihema chopatulikacho.

  • Numeri 16:42
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 42 Khamulo litasonkhana pamodzi kuti liukire Mose ndi Aroni, linacheukira kuchihema chokumanako. Anthuwo anangoona kuti mtambo waphimba chihemacho, ndipo ulemerero wa Yehova wayamba kuonekera.+

  • 1 Mafumu 8:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Tsopano ansembe atatuluka m’malo oyera, mtambo+ unadzaza nyumba ya Yehova.

  • Chivumbulutso 15:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Ndipo malo opatulikawo anadzaza utsi chifukwa cha ulemerero wa Mulungu,+ ndiponso chifukwa cha mphamvu zake. Palibe amene anatha kulowa m’malo opatulikawo, mpaka miliri 7+ ya angelo 7 aja itatha.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena