Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 11:44
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 44 Ine ndine Yehova Mulungu wanu.+ Mudzipatule ndi kukhala oyera,+ chifukwa ine ndine woyera.+ Choncho musamadzidetse ndi chamoyo chilichonse choyenda padziko lapansi.

  • Levitiko 18:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Chotero muzisunga malamulo anga kuti musamachite iliyonse mwa miyambo yonyansa imene anthu akhala akuchita inu musanafike.+ Pamenepo mudzapewa kudzidetsa ndi miyamboyo. Ine ndine Yehova Mulungu wanu.’”

  • Levitiko 19:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 “Uza khamu lonse la ana a Isiraeli kuti, ‘Mukhale oyera,+ chifukwa ine Yehova Mulungu wanu ndine woyera.+

  • Ezekieli 20:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Uwauze kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Pa tsiku limene ndinasankha Isiraeli,+ ndinakweza mkono wanga+ polumbirira mbewu ya nyumba ya Yakobo+ ndi kuwachititsa kuti andidziwe m’dziko la Iguputo.+ Inde, ndinakweza mkono wanga ndi kuwalumbirira kuti, ‘Ine ndine Yehova Mulungu wanu.’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena