Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 27:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Upange nyanga m’makona ake anayi. Nyanga+ zakezo zituluke m’makona akewo, ndipo ulikute ndi mkuwa.+

  • Ekisodo 37:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Kenako anapanga guwa lansembe zofukiza+ la matabwa a mthethe.+ M’litali mwake linali mkono umodzi, m’lifupi mwake mkono umodzi. Mbali zake zonse zinayi zinali zofanana, ndipo msinkhu wake unali mikono iwiri. Guwalo linali ndi nyanga pamwamba pake.+

  • Levitiko 4:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Wansembeyo azipaka ena mwa magaziwo panyanga+ za guwa lansembe la zofukiza zonunkhira pamaso pa Yehova, limene lili m’chihema chokumanako. Magazi ena onse a ng’ombeyo aziwathira pansi+ pa guwa lansembe zopsereza, limene lili pakhomo la chihema chokumanako.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena