Ekisodo 37:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndiyeno analikuta ndi golide woyenga bwino pamwamba pake ndi m’mbali mwake kuzungulira guwalo, komanso nyanga zake. Analipangira mkombero wagolide wozungulira guwa lonselo.+
26 Ndiyeno analikuta ndi golide woyenga bwino pamwamba pake ndi m’mbali mwake kuzungulira guwalo, komanso nyanga zake. Analipangira mkombero wagolide wozungulira guwa lonselo.+