Levitiko 16:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Ndiyeno khamu la ana a Isiraeli+ lizim’patsa ana a mbuzi awiri, amphongo, kuti akhale nsembe yamachimo,+ ndi nkhosa yamphongo imodzi kuti ikhale nsembe yopsereza.+ Levitiko 16:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Ndiponso Aroni azitenga ng’ombe yamphongo ya nsembe yake yamachimo,+ ndipo aziphimba machimo+ ake+ ndi a nyumba yake.+ Levitiko 16:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ena mwa magaziwo aziwadonthezera+ paguwalo ndi chala chake maulendo 7, kuti aliyeretse ku zodetsa za ana a Isiraeli ndi kulipatula.
5 “Ndiyeno khamu la ana a Isiraeli+ lizim’patsa ana a mbuzi awiri, amphongo, kuti akhale nsembe yamachimo,+ ndi nkhosa yamphongo imodzi kuti ikhale nsembe yopsereza.+
6 “Ndiponso Aroni azitenga ng’ombe yamphongo ya nsembe yake yamachimo,+ ndipo aziphimba machimo+ ake+ ndi a nyumba yake.+
19 Ena mwa magaziwo aziwadonthezera+ paguwalo ndi chala chake maulendo 7, kuti aliyeretse ku zodetsa za ana a Isiraeli ndi kulipatula.