Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 24:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Davide atawerengadi anthuwo anavutika mumtima mwake.+ Choncho Davide anauza Yehova kuti: “Ndachimwa+ kwambiri pochita zimene ndachitazi. Tsopano Yehova, khululukani cholakwa cha ine mtumiki wanu+ chonde, pakuti ndachita chinthu chopusa kwambiri.”+

  • 2 Samueli 24:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Pamenepo Yehova anagwetsa mliri+ mu Isiraeli kuyambira m’mawa mpaka nthawi yoikidwiratu, moti pa anthu onse kuyambira ku Dani mpaka ku Beere-seba+ panafa anthu 70,000.+

  • 1 Mbiri 21:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Zaka zitatu za njala+ kapena miyezi itatu yoti adani anu akuseseni+ ndi kukuphani ndi lupanga lawo, kapenanso masiku atatu a lupanga la Yehova,+ lomwe ndi mliri+ umene udzagwe m’dziko lanu mpaka mngelo wa Yehova atasakaza+ madera onse a Isiraeli.’ Ndiye tandiuzani zoti ndikayankhe kwa Amene wanditumayo.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena