Miyambo 7:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndawaza pabedi panga zonunkhiritsa za mule, aloye ndi sinamoni.+ Chivumbulutso 18:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Komanso palibe wowagula sinamoni, amomo,* zofukiza, mafuta onunkhira, lubani, vinyo, mafuta a maolivi, ufa wabwino kwambiri, tirigu, ng’ombe, nkhosa, mahatchi, ngolo, akapolo, ndi anthu.+
13 Komanso palibe wowagula sinamoni, amomo,* zofukiza, mafuta onunkhira, lubani, vinyo, mafuta a maolivi, ufa wabwino kwambiri, tirigu, ng’ombe, nkhosa, mahatchi, ngolo, akapolo, ndi anthu.+