Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 29:40
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 40 Popereka mwana wa nkhosa woyamba, uzipereka limodzi ndi ufa wosalala,+ muyezo wake gawo limodzi mwa magawo 10 a muyezo wa efa,* wothira mafuta oyenga bwino kwambiri okwana gawo limodzi mwa magawo anayi a muyezo wa hini,* ndi gawo limodzi mwa magawo anayi a vinyo wa nsembe yachakumwa.+

  • Levitiko 19:36
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 36 Muzikhala ndi masikelo olondola,+ miyala yolondola yoyezera kulemera kwa zinthu, muyezo wolondola wa efa ndi muyezo wolondola wa hini.* Ine ndine Yehova Mulungu wanu, amene ndinakutulutsani m’dziko la Iguputo.

  • Numeri 15:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Ndipo muzikapereka vinyo monga nsembe yachakumwa.+ Azikakhala wokwanira gawo limodzi mwa magawo anayi a muyezo wa hini. Vinyoyo muzikam’pereka limodzi ndi nsembe yopsereza, kapena ndi nsembe ya mwana wa nkhosa wamphongo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena