Ekisodo 37:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Kuwonjezera pamenepo, anapanganso mafuta ogwiritsa ntchito pa kudzoza kopatulika,+ ndi mafuta onunkhira+ osakaniza mwaluso. 1 Mafumu 1:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Tsopano wansembe Zadoki anatenga nyanga ya mafuta+ m’chihema+ n’kudzoza+ Solomo. Ndiyeno anthuwo anayamba kuliza lipenga ndipo anthu onse anafuula kuti: “Mfumu Solomo ikhale ndi moyo wautali!”+ Salimo 89:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndapeza Davide mtumiki wanga,+Ndipo ndamudzoza ndi mafuta anga opatulika.+
29 Kuwonjezera pamenepo, anapanganso mafuta ogwiritsa ntchito pa kudzoza kopatulika,+ ndi mafuta onunkhira+ osakaniza mwaluso.
39 Tsopano wansembe Zadoki anatenga nyanga ya mafuta+ m’chihema+ n’kudzoza+ Solomo. Ndiyeno anthuwo anayamba kuliza lipenga ndipo anthu onse anafuula kuti: “Mfumu Solomo ikhale ndi moyo wautali!”+