Ekisodo 35:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 choikapo nyale+ zounikira ndi zipangizo zake, nyale zake, ndi mafuta+ a nyalezo. Ekisodo 37:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kenako anapanga choikapo nyale+ chagolide woyenga bwino. Chimenechi chinali chosula. Choikapo nyalechi chinali ndi nthambi m’mbali mwake, ndiponso chinali ndi masamba ofunga duwa, mfundo ndi maluwa.+
17 Kenako anapanga choikapo nyale+ chagolide woyenga bwino. Chimenechi chinali chosula. Choikapo nyalechi chinali ndi nthambi m’mbali mwake, ndiponso chinali ndi masamba ofunga duwa, mfundo ndi maluwa.+