Ekisodo 30:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Zinthu zimenezi upangire mafuta ogwiritsa ntchito pa kudzoza kopatulika, mafuta onunkhira osakaniza mwaluso.+ Akhale mafuta ogwiritsa ntchito pa kudzoza kopatulika.+ Ekisodo 30:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Zinthu zimenezi upangire zofukiza,+ msanganizo wa zonunkhiritsa zosakaniza mwaluso, wothira mchere,+ msanganizo weniweni wopatulika. Ekisodo 37:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Kuwonjezera pamenepo, anapanganso mafuta ogwiritsa ntchito pa kudzoza kopatulika,+ ndi mafuta onunkhira+ osakaniza mwaluso.
25 Zinthu zimenezi upangire mafuta ogwiritsa ntchito pa kudzoza kopatulika, mafuta onunkhira osakaniza mwaluso.+ Akhale mafuta ogwiritsa ntchito pa kudzoza kopatulika.+
35 Zinthu zimenezi upangire zofukiza,+ msanganizo wa zonunkhiritsa zosakaniza mwaluso, wothira mchere,+ msanganizo weniweni wopatulika.
29 Kuwonjezera pamenepo, anapanganso mafuta ogwiritsa ntchito pa kudzoza kopatulika,+ ndi mafuta onunkhira+ osakaniza mwaluso.