Ekisodo 32:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Mose ali m’phirimo, anthu anaona kuti akuchedwa kutsika.+ Chotero anthuwo anasonkhana kwa Aroni ndi kumuuza kuti: “Tipangire mulungu woti atitsogolere,+ chifukwa sitikudziwa zimene zachitikira Mose, amene anatitulutsa m’dziko la Iguputo.”+ Deuteronomo 4:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Chotero musamale moyo wanu,+ chifukwa pa tsiku limene Yehova analankhula nanu kuchokera pakati pa moto ku Horebe, simunaone kalikonse+ m’motomo. Machitidwe 7:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Anauza Aroni kuti, ‘Tipangire milungu ititsogolere. Chifukwa sitikudziwa zimene zachitikira Mose, amene anatitsogolera potuluka m’dziko la Iguputo.’+ Machitidwe 17:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 “Popeza kuti ndife mbadwa za Mulungu,+ tisaganize kuti Mulunguyo+ ali ngati golide, siliva, mwala kapena chilichonse chosemedwa mwa luso ndi nzeru za munthu.+
32 Mose ali m’phirimo, anthu anaona kuti akuchedwa kutsika.+ Chotero anthuwo anasonkhana kwa Aroni ndi kumuuza kuti: “Tipangire mulungu woti atitsogolere,+ chifukwa sitikudziwa zimene zachitikira Mose, amene anatitulutsa m’dziko la Iguputo.”+
15 “Chotero musamale moyo wanu,+ chifukwa pa tsiku limene Yehova analankhula nanu kuchokera pakati pa moto ku Horebe, simunaone kalikonse+ m’motomo.
40 Anauza Aroni kuti, ‘Tipangire milungu ititsogolere. Chifukwa sitikudziwa zimene zachitikira Mose, amene anatitsogolera potuluka m’dziko la Iguputo.’+
29 “Popeza kuti ndife mbadwa za Mulungu,+ tisaganize kuti Mulunguyo+ ali ngati golide, siliva, mwala kapena chilichonse chosemedwa mwa luso ndi nzeru za munthu.+