Yoswa 22:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Wamphamvu,+ Mulungu,+ Yehova,+ Wamphamvu, Mulungu, Yehova, iye akudziwa,+ ndipo nayenso Isiraeli adziwa.+ Ngati tachita zimenezi chifukwa chopanduka+ ndiponso chifukwa cha kusakhulupirika pamaso pa Yehova,+ musatisiye amoyo lero. Salimo 50:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Wamphamvuyo,+ Yehova, Mulungu,+ walankhula+Ndipo akuitana dziko lapansi,+Kuchokera kotulukira dzuwa mpaka kumene limalowera.+ Yesaya 46:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kumbukirani zinthu zoyambirira zimene zinachitika kalekale,+ kuti ine ndine Mulungu+ ndipo palibenso Mulungu wina,+ kapena aliyense wofanana ndi ine.+
22 “Wamphamvu,+ Mulungu,+ Yehova,+ Wamphamvu, Mulungu, Yehova, iye akudziwa,+ ndipo nayenso Isiraeli adziwa.+ Ngati tachita zimenezi chifukwa chopanduka+ ndiponso chifukwa cha kusakhulupirika pamaso pa Yehova,+ musatisiye amoyo lero.
50 Wamphamvuyo,+ Yehova, Mulungu,+ walankhula+Ndipo akuitana dziko lapansi,+Kuchokera kotulukira dzuwa mpaka kumene limalowera.+
9 Kumbukirani zinthu zoyambirira zimene zinachitika kalekale,+ kuti ine ndine Mulungu+ ndipo palibenso Mulungu wina,+ kapena aliyense wofanana ndi ine.+