Ekisodo 23:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “Tsopano ndikukutumizira mngelo+ wokutsogolera kuti akuteteze m’njira ndi kukakulowetsa m’dziko limene ndakukonzera.+ Ekisodo 32:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Tsopano atsogolere anthuwa kumalo amene ndakuuza. Taona! Mngelo wanga akhala patsogolo panu,+ ndipo pa tsiku langa lopereka chilango, ndidzawalangadi chifukwa cha tchimo lawo.”+
20 “Tsopano ndikukutumizira mngelo+ wokutsogolera kuti akuteteze m’njira ndi kukakulowetsa m’dziko limene ndakukonzera.+
34 Tsopano atsogolere anthuwa kumalo amene ndakuuza. Taona! Mngelo wanga akhala patsogolo panu,+ ndipo pa tsiku langa lopereka chilango, ndidzawalangadi chifukwa cha tchimo lawo.”+