Genesis 42:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Atafika pamalo ogona, mmodzi wa iwo anamasula thumba lake kuti atengemo chakudya chopatsa bulu wake.+ Atamasula, anangoona kuti ndalama zake zili pakamwa pa thumbalo.+ Yeremiya 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndikanakonda kukhala ndi malo a m’chipululu ogona anthu apaulendo.+ Pamenepo ndikanasiya anthu anga ndi kuwachokera, pakuti onsewo ndi achigololo,+ gulu la anthu ochita zachinyengo.+
27 Atafika pamalo ogona, mmodzi wa iwo anamasula thumba lake kuti atengemo chakudya chopatsa bulu wake.+ Atamasula, anangoona kuti ndalama zake zili pakamwa pa thumbalo.+
2 Ndikanakonda kukhala ndi malo a m’chipululu ogona anthu apaulendo.+ Pamenepo ndikanasiya anthu anga ndi kuwachokera, pakuti onsewo ndi achigololo,+ gulu la anthu ochita zachinyengo.+